Mawu a M'munsi
c Koma anthu amene adzaukitsidwe kuti akhale padzikoli adzakhala ndi moyo wosatha osati moyo umene sungafe kapena kuwonongeka. Kuti muone kusiyana pakati pa moyo wosatha ndi moyo umene sungafe kapena kuwonongeka, werengani Nsanja ya Olonda yachingelezi ya April 1, 1984, tsamba 30 ndi 31.