Mawu a M'munsi
a Pa nkhani ya zimene asayansi akuchita kuti amvetse chifukwa chake timakalamba n’kufa, buku lakuti Insight on the Scriptures limati: “Iwo amalephera kuzindikira kuti Mlengi wathu ndi amene anapereka chilango cha imfa. Choncho n’zosatheka kuti amvetse zimene zimachitika.”—Voliyumu 2, tsamba 247.