Mawu a M'munsi
g Yesu analosera zimene zidzachitike m’masiku otsiriza kuti: “Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu [amene akuimira ulamuliro wa Mulungu], kufikira nthawi zoikidwiratu za anthu a mitundu inawo zitakwanira.” (Luka 21:24) Choncho, pa nthawi imene Yesu anali padziko lapansili, ulamuliro wa Mulungu unali udakali wosokonekera mpaka nthawi ya mapeto.