Mawu a M'munsi
a Baibulo limasonyeza kuti Yosefe anali ndi zaka 17 kapena 18 pamene anayamba kutumikira panyumba ya Potifara ndipo anakhalako kwa zaka zingapo. Zimenezi zikusonyeza kuti mmene ankapita kundende n’kuti ali ndi zaka zoposa 20. Baibulo limasonyeza kuti anatuluka kundende ali ndi zaka 30.—Genesis 37:2; 39:6; 41:46.