Mawu a M'munsi
a Kuti mupeze munthu woti aziphunzira nanu Baibulo kapena kuti mudziwe komwe Nyumba ya Ufumu ili m’dera lanu, lankhulani ndi munthu amene anakupatsani magaziniyi kapena pitani pa webusaiti yathu ya www.pr418.com/ny. Pitani pamene palembedwa kuti POYAMBIRA › TIPEZENI pamunsi pa tsambalo.