Mawu a M'munsi
a Nkhani zoterezi zachitikanso m’mayiko monga ku Argentina (onani Buku Lapachaka lachingelezi la 2001, tsamba 186); ku East Germany (onani Buku Lapachaka lachingelezi la 1999, tsamba 83); ku Papua New Guinea (onani Buku Lapachaka lachingelezi la 2005, tsamba 63) ndiponso kuchilumba cha Robinson Crusoe (onani Nsanja ya Olonda ya June 15, 2000, tsamba 9).