Mawu a M'munsi
b Mawu akuti “Beteli” amatanthauza “Nyumba ya Mulungu.” A Mboni za Yehova amagwiritsa ntchito mawuwa ponena za maofesi awo omwe ali m’mayiko osiyanasiyana. (Genesis 28:17, 19) Anthu amene amatumikira pa Beteli amagwira ntchito zosiyanasiyana. Ntchitozi zimathandiza kuti ntchito yolalikira, yomwe a Mboni za Yehova amagwira, iziyenda bwino.