Mawu a M'munsi
c Odzozedwa amene adzakhalapo pa nthawiyo sadzatengedwa kupita kumwamba ndi matupi awo. (1 Akor. 15:48, 49) Zimene zidzachitikire matupi awo n’zofanana ndi zimene zinachitikira thupi la Yesu.