Mawu a M'munsi d Salimo 45 limasonyezanso mmene zinthuzi zidzachitikire. Limasonyeza kuti choyamba, Mfumu idzamenya nkhondo kenako ukwati udzachitika.