Mawu a M'munsi
a Ufumu wa Mulungu udzathetsanso imfa. Mungawerenge nkhani yakuti ”Kuyankha Mafunso a M’Baibulo” m’magazini ino, yomwe ikusonyeza kuti Mulungu adzaukitsa anthu ambirimbiri amene anamwalira, kuphatikizapo amene anaphedwa pa nkhondo.