Mawu a M'munsi
b Mipukutu yomwe inapezeka ku Nyanja Yakufa inalembedwa zaka zoposa 1,000, Amasorete asanayambe kukopera Malemba. Zimene Amasorete anakopera ndi zomwe zinagwiritsidwa ntchito pomasulira Baibulo la Dziko Latsopano.