Mawu a M'munsi
b Patapita zaka 5 mu 1535, womasulira wina wachifulenchi dzina lake Olivétan anatulutsa Baibulo lake lomasuliridwa kuchokera ku zinenero zoyambirira za Baibulo. Pomasulira Malemba Achigiriki anadalira kwambiri zimene Lefèvre analemba.