Mawu a M'munsi
a Kuti mumve zambiri zokhudza zizindikiro za masiku otsiriza, onani mutu 9 wakuti, “Kodi Dzikoli Lithadi Posachedwa?” m’buku lakuti, Zimene Baibulo Limaphunzitsa, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova. Bukuli likupezekanso pawebusaiti ya www.jw.org/ny.