Mawu a M'munsi
b Akhristu odzozedwa okhulupirika sadzafunika kulandira nawo chizindikirochi. M’malomwake iwo amadindidwa chidindo komaliza akatsala pang’ono kumwalira kapena adzadindidwa chisautso chachikulu chitatsala pang’ono kuyamba.—Chiv. 7:1, 3.