Mawu a M'munsi
b Nkhani ya nkhondoyi inafotokozedwa m’buku lina limene linatuluka mu 1904 (Millennial Dawn, Volume VI) komanso mu Nsanja ya Olonda yachijeremani ya August 1906. Nsanja ya Olonda ya September 1915 inafotokoza bwinobwino zoyenera kuchita ndipo inasonyeza kuti Ophunzira Baibulo sayenera kulowa usilikali. Koma nkhani imeneyi sinatuluke m’magazini yachijeremani.