Mawu a M'munsi
a Wolemba mbiri wina dzina lake James Parkes anati: “Ayuda . . . anali ndi ufulu wochita zikondwerero zawo zonse. Ufulu umenewu sunkaperekedwa kwa Ayuda okha. Tikutero chifukwa chakuti Aroma ankayesetsa kupereka ufulu kwa anthu okhala m’madera osiyanasiyana amene ankalamulira.”