Mawu a M'munsi
a Poyamba mayina awo anali Abulamu ndi Sarai. Koma kenako Yehova anawapatsa mayina akuti Abulahamu ndi Sara ndipo anayamba kudziwika kwambiri ndi mayina amenewa.—Genesis 17:5, 15.