Mawu a M'munsi
b Pa nthawiyo Yehova ankalola mitala komanso kukhala ndi akazi apambali. Koma patapita nthawi anapatsa Yesu Khristu mphamvu kuti abwezeretse lamulo lokhudza ukwati, lomwe linalipo m’munda wa Edeni. Lamulo lake linali loti mwamuna azikhala ndi mkazi mmodzi.—Genesis 2:24; Mateyu 19:3-9.