Mawu a M'munsi c Sara ndi mkazi yekhayo amene Baibulo limatchula kuti anali ndi zaka zingati pamene ankamwalira.