Mawu a M'munsi
a Anthu ambiri amakonda kupatsa ena mphatso pa tsiku lobadwa kapena pa zikondwerero zina. Koma zimene zimachitika pa zikondwerero zimenezi nthawi zambiri zimakhala zosemphana ndi zimene Baibulo limaphunzitsa. Kuti mudziwe zambiri, werengani nkhani yakuti, “Zimene Owerenga Amafunsa—Kodi Akhristu Ayenera Kukondwerera Khirisimasi?” yomwe ili m’magaziniyi.