Mawu a M'munsi
a Ngati mukufuna kudziwa zambiri zokhudza mmene miyambo yomwe imachitika pa Khirisimasi inayambira, werengani nkhani yakuti, “Zimene Owerenga Amafunsa . . . Kodi ndi Zinthu Ziti Zomwe Tiyenera Kudziwa pa Nkhani ya Khirisimasi?” mu Nsanja ya Olonda ya December 1, 2014. Magaziniyi ikupezekanso pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.