Mawu a M'munsi a Yesu sananene ngati mtumikiyo anachitadi zimene anamunenezazo. Mawu achigiriki amene anamasuliridwa kuti ‘kuneneza’ pa Luka 16:1 angatanthauze kunamizira munthu. Ndipo mfundo yaikulu ya Yesu inagona pa zimene mtumikiyo anachita atanenezedwa, osati chifukwa chimene anamuchotsera ntchito.