Mawu a M'munsi
a Bungwe loona zaumoyo ku England linanena kuti: “Malupu okhala ndi mkuwa wambiri amathandiza kwambiri kuti mayi asatenge pakati moti pa akazi 100 amene amagwiritsa ntchito malupuwa pachaka, mmodzi yekha ndi amene angatenge pakati ndipo mwina palibenso amene angatenge. Koma malupu amene amakhala ndi mkuwa wochepa, mphamvu yake imakhalanso yocheperapo.”