Mawu a M'munsi
b Madokotala ena amauza akazi amene amataya magazi ambiri pa nthawi yosamba kuti azigwiritsanso ntchito malupu amenewa chifukwa amathandiza kuti asamataye magazi ambiri. Amanena zimenezi kwa akazi a pa banja ngakhalenso amene sali pa banja.