Mawu a M'munsi
b A Mboni za Yehova amaphunzira Baibulo ndi anthu pofuna kuwathandiza kuti ayambe kumvetsa bwino Malemba. Kuti mudziwe zambiri zokhudza mmene phunziro la Baibulo limachitikira, onerani vidiyo yakuti, Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? Kuti mupeze vidiyoyi, pitani pa webusaiti ya jw.org/ny (Pitani pamene alemba kuti MABUKU > MAVIDIYO).