Mawu a M'munsi
b Panopa inalowedwa m’malo ndi Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu. Atumiki a nthawi zonse oyenerera amene akutumikira m’dziko lina akhoza kufunsira kuti alowe sukuluyi m’dziko lawo kapena m’dziko lina kumene imachitika m’chilankhulo chawo.