Mawu a M'munsi
a Ngakhale Yesu anazindikira kuti zimakhala zovuta kuti munthu azilalikira m’dera la kwawo. Ndipo mfundo imeneyi inatchulidwa ndi anthu 4 onse amene analemba Uthenga Wabwino.—Mat. 13:57; Maliko 6:4; Luka 4:24; Yoh. 4:44.