Mawu a M'munsi
c N’zoona kuti “kubereka zipatso” kungatanthauzenso kukhala ndi “makhalidwe amene mzimu woyera umatulutsa.” Koma munkhaniyi ndiponso yotsatira tikambirana kwambiri za “chipatso cha milomo yathu,” kapena kuti kulalikira za Ufumu.—Agal. 5:22, 23; Aheb. 13:15.