Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Mawu oti “abale” angagwiritsidwenso ntchito ponena za alongo. Mwachitsanzo, Paulo ananena m’kalata yake yopita kwa Aroma kuti akulembera “abale.” Koma mawu amenewa ankatanthauzanso alongo chifukwa ena mwa alongowo anawatchula mayina awo. (Aroma 16:3, 6, 12) Ndipotu Nsanja ya Olonda yakhala ikugwiritsa ntchito mawu oti ‘abale ndi alongo’ pofotokoza za Akhristu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena