Mawu a M'munsi
a Yosefe atatuluka mundende, anaona kuti Yehova anamulimbikitsa pomupatsa mwana wamwamuna. Iye anapatsa mwanayo dzina lakuti Manase ndipo anati: “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse.”—Gen. 41:51, mawu am’munsi.