Mawu a M'munsi
a Koma chimene anthuwa sadziwa n’chakuti ngakhale munthu amene amayendera maganizo akeake amakhala akutsatira winawake. Kaya munthu akuganizira nkhani zikuluzikulu monga mmene moyo unayambira kapena zing’onozing’ono monga kavalidwe, sangapeweretu kuyendera maganizo a anthu ena. Koma aliyense akhoza kusankha kuti aziyendera maganizo a ndani.