Mawu a M'munsi
d MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: Mlongo akuchita chitsanzo cha ulendo wobwereza pamisonkhano. Pambuyo pake, tcheyamani akumupatsa malangizo ndipo mlongoyo akulemba malangizowo m’kabuku kakuti Kuphunzitsa. Kumapeto kwa mlungu, mlongoyu ali mu utumiki ndipo akugwiritsa ntchito zimene anaphunzira kumisonkhano.