Mawu a M'munsi
a Anthu amene anagwiriridwa ali ana amavutikabe ngakhale patapita zaka zambiri. Nkhaniyi itithandiza kumvetsa chifukwa chake zili choncho. Tikambirananso kuti ndi ndani amene angalimbikitse anthu amenewa. Pomaliza, tikambirana zimene tingachite kuti tiwalimbikitse.