Mawu a M'munsi
c MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: M’bale akufufuza kuti amudziwe bwino Amosi amene analemba buku la m’Baibulo. Zithunzi zomwe zili kumbuyo kwake zikusonyeza zimene m’baleyo akuona m’maganizo ake pamene akuwerenga ndiponso kusinkhasinkha nkhaniyi.