Mawu a M'munsi
d Akulu sayenera kupempha kuti mwana amene wagwiriridwa akhalepo pamene akulankhula ndi munthu amene wamugwirirayo. Ndi bwino kuti makolo kapena munthu wina amene mwanayo amamudalira afotokozere akulu zimene mwanayo akunena. Izi zingathandize kuti maganizo a mwanayo asapitirize kusokonezeka.