Mawu a M'munsi
d MAWU OFOTOKOZERA ZITHUNZI: Mlongo wapita kuyunivesite. Iye ndi anzake akopeka ndi maganizo a mphunzitsi wawo oti asayansi akhoza kuthetsa mavuto a mādzikoli. Kenako wapita ku Nyumba ya Ufumu koma sizikumusangalatsa ndipo akungopezera anthu zifukwa.