Mawu a M'munsi
a Loti, Yobu ndi Naomi ankatumikira Yehova mokhulupirika koma onsewa anakumana ndi mavuto amene ankawadetsa nkhawa. Munkhaniyi tikambirana zimene tingaphunzire kwa anthu amenewa. Tikambirananso chifukwa chake tiyenera kukhala oleza mtima, achifundo komanso olimbikitsa kwa abale ndi alongo amene akukumana ndi mavuto.