Mawu a M'munsi
b Mawu akuti Kitawala anachokera ku mawu achiswahili amene amatanthauza “kulamulira kapena kutsogolera.” Cholinga cha gululi chinali chokhudza ndale chifukwa linkafuna kuti anthu amasuke ku ulamuliro wa dziko la Belgium. Gulu la Kitawala linkapeza mabuku a Mboni za Yehova, kuwaphunzira komanso kuwafalitsa koma linkasintha mfundo za m’Baibulo kuti zigwirizane ndi maganizo awo pa nkhani za ndale, zikhulupiriro zawo komanso khalidwe lawo loipa.