Mawu a M'munsi
a Masiku ano, timakumana ndi anthu ambiri omwe sali m’chipembedzo chilichonse. Munkhaniyi tikambirana zimene tingachite kuti tiwalalikire komanso kuwathandiza kuti ayambe kukhulupirira Yehova Mulungu ndiponso Baibulo.