Mawu a M'munsi
a Masiku ano, tiyenera kukonda kwambiri abale athu kusiyana ndi m’mbuyo monsemu. Kalata imene Paulo analembera Afilipi ingatithandize kudziwa zimene tingachite kuti chikondi chathu chizikula ngakhale kuti tikukumana ndi mavuto.