Mawu a M'munsi
a Khalidwe lina lofunika limene tiyenera kukhala nalo ndi kudzichepetsa. Kodi kudzichepetsa n’kutani? N’chifukwa chiyani tiyenera kukhala odzichepetsa? Nanga n’chifukwa chiyani tingavutike kukhala odzichepetsa zinthu zikasintha pa moyo wathu? Munkhaniyi tikambirana mafunso amenewa.