Mawu a M'munsi
a Tonsefe timakonda kwambiri kutumikira Yehova. Koma kodi ndife odzipereka kwa iye yekha? Yankho la funsoli lingadalire zinthu zimene timasankha pa moyo wathu. Tiyeni tikambirane zinthu ziwiri zimene zingatithandize kudziwa ngati ndife odzipereka kwa Yehova yekha kapena ayi.