Mawu a M'munsi
a Yehova anakonza njira yapadera yothandizira Aisiraeli kuti azikhala pa ufulu. Iye anakonza zoti pazikhala Chaka cha Ufulu. Akhristufe sititsatira Chilamulo cha Mose, koma kuphunzira za Chaka cha Ufulu kungatithandize kwambiri. Munkhaniyi tiona kuti Chaka cha Ufulu chimatikumbutsa zimene Yehova watikonzera komanso mmene zinthuzo zingatithandizire.