Mawu a M'munsi
a KachiƔirinso chimenechi ndicho chiƔerengero chapamwamba chatsopano chimene chikusonyeza kuwonjezeka kwa 14 peresenti kuposa chaka chatha chautumiki. Ndithudi Yehova akudalitsa ntchito imene mipingo ikuchita. Tikukuthokozani abale ndi alongo!