Mawu a M'munsi a b Dziwani izi: Kuyambira mwezi uno, Ndandanda ya Utumiki izikhala ndi phunziro limene wophunzira wapatsidwa lomwe lizikhala kutsogolo kwa nkhani yake mumkutira mawu. Phunziroli lizichokera m’kabuku kakuti Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso (th).