Mawu a M'munsi
a Kodi munakumanapo ndi mavuto amene anakupangitsani kumva kuti ndinu wachabechabe? Nkhaniyi ikuthandizani kukumbukira kuti Yehova amaona kuti ndinu amtengo wapatali kwambiri. Ifotokoza zimene mungachite kuti musamadzione kuti ndinu wachabechabe ngakhale mutakumana ndi zinthu zokhumudwitsa.