Mawu a M'munsi
a Kodi inuyo mukufuna kubatizidwa? Ngati ndi choncho, nkhaniyi yakonzedwa kuti ikuthandizeni. Tikambirana mafunso ofunika kwambiri pa nkhani imeneyi. Zimene mungayankhe pa mafunsowo zingakuthandizeni kudziwa ngati mwakonzekadi kuti mubatizidwe.