Mawu a M'munsi
a Kodi mmene timaonera anthu am’gawo lathu zimakhudza bwanji mmene timalalikirira komanso kuphunzitsa? Munkhaniyi tiona mmene Yesu ndi Paulo ankaonera anthu. Tikambirananso zimene tingachite kuti tiziwatsanzira poganizira zimene anthu amakhulupirira, zimene amakonda komanso powaona kuti akhoza kukhala ophunzira a Khristu.