Mawu a M'munsi
c MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI Tsamba 10-11: Banja likulalikira kunyumba ndi nyumba ndipo laona (1) nyumba yosamaliridwa bwino, yokhala ndi maluwa; (2) nyumba ya banja limene lili ndi ana aang’ono; (3) nyumba yauve kunja ndi mkati momwe komanso (4) nyumba ya anthu achipembedzo. Kodi ndi nyumba iti imene mungapeze munthu yemwe angadzakhale wophunzira?