Mawu a M'munsi
a Anthufe si angwiro ndipo timafulumira kuweruza anthu ena komanso zolinga zawo. Koma Yehova “amaona mmene mtima ulili.” (1 Sam. 16:7) Munkhaniyi tikambirana zimene Yehova anachita pothandiza Yona, Eliya, Hagara komanso Loti. Zimenezi zitithandiza kuti tizimutsanzira pochita zinthu ndi abale ndi alongo athu.